spot_img
Sunday, October 13, 2024
More
    HomeLatestROAD TO 2025: Nthumwi za PDF zafika ku Blantyre

    ROAD TO 2025: Nthumwi za PDF zafika ku Blantyre

    -

    Nthumwi zambiri za ku msonkhano waukulu wa chipani cha PDP tsopano zafika mu Holo ya Comesa mu mzinda wa Blantyre.

    kondwani Nankhumwa, yemwe ndi mtsogoleri wa PDP, akuyembekezereka kusegulira msonkhano’wu.

    Mlembi wa mkulu wa chipanichi, a Simeon Phiri wati msonkhanowu uyamba posachedwapa.

    Ku msonkhanowu kukuyembekeza kukhala nthumwi 1, 200 zochokera m’madera onse a m’dziko lino.

    Related articles

    LEAVE A REPLY

    Please enter your comment!
    Please enter your name here

    spot_img

    Latest posts